Mateyu 27:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo iye anataya pansi ndalamazo pa Kachisi, nachokapo, nadzipachika yekha pakhosi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo iye anataya pansi ndalamazo pa Kachisi, nachokapo, nadzipachika yekha pakhosi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Yudasi adakaziponya ndalamazo m'Nyumba ya Mulungu nachokapo, kenaka nkukadzikhweza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pamenepo Yudasi anaponya ndalamazo mʼNyumba ya Mulungu nachoka. Kenaka anapita nakadzimangirira. Onani mutuwo |