Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 27:45 - Buku Lopatulika

45 Ndipo ora lachisanu ndi chimodzi panali mdima padziko lonse, kufikira ora lachisanu ndi chinai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

45 Ndipo ora lachisanu ndi chimodzi panali mdima pa dziko lonse, kufikira ora lachisanu ndi chinai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

45 Kuyambira pa 12 koloko masana mpaka pa 3 koloko, padaagwa mdima pa dziko lonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

45 Kuyambira 12 koloko masana mpaka 3 koloko, kunachita mdima pa dziko lonse.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 27:45
9 Mawu Ofanana  

Ndiveka thambo ndi kuda, ndi kuyesa chiguduli chofunda chake.


Ndipo kudzachitika tsiku lomwelo, ati Ambuye Yehova, ndidzalowetsa dzuwa usana, ndi kudetsa dziko pausana poyera.


Ndipo panali ora lachitatu, ndipo anampachika Iye.


Koma linali tsiku lokonza Paska; panali monga ora lachisanu ndi chimodzi. Ndipo ananena kwa Ayuda, Taonani, mfumu yanu!


Koma Petro ndi Yohane analikukwera kunka ku Kachisi pa ora lakupembedza, ndilo lachisanu ndi chinai.


Ndipo mngelo wachinai anaomba lipenga, ndipo limodzi la magawo atatu a dzuwa linagwidwa, ndi limodzi la magawo atatu a mwezi, ndi limodzi la magawo atatu a nyenyezi; kuti limodzi la magawo ao atatu lidetsedwe, ndi kuti limodzi la magawo ake atatu a usana lisawale, ndi usiku momwemo.


Ndipo anatsegula pa chiphompho chakuya; ndipo unakwera utsi wotuluka m'chiphomphomo, ngati utsi wa ng'anjo yaikulu; ndipo dzuwa ndi thambo zinada, chifukwa cha utsiwo wa kuchiphomphocho.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa