Mateyu 27:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo iye anati, Chifukwa ninji? Anachita choipa chotani? Koma iwo anafuulitsa kopambana, Apachikidwe pamtanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo iye anati, Chifukwa ninji? Anachita choipa chotani? Koma iwo anafuulitsa kopambana, Apachikidwe pamtanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pilato adaŵafunsanso kuti, “Adalakwanji?” Koma anthu aja adafuula koposa kuti, “Apachikidwe pa mtanda!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pilato anafunsa kuti, “Chifukwa chiyani? Wachita choyipa chotani?” Koma anachita phokoso nafuwula kwambiri kuti, “Mpachikeni!” Onani mutuwo |