Mateyu 27:18 - Buku Lopatulika18 Pakuti anadziwa kuti anampereka Iye mwanjiru. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pakuti anadziwa kuti anampereka Iye mwanjiru. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Adaatero chifukwa adaadziŵa kuti Yesuyo anthuwo angodzampereka chifukwa cha kaduka chabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pakuti anadziwa kuti anamupereka Yesu chifukwa cha kaduka. Onani mutuwo |