Mateyu 27:10 - Buku Lopatulika10 ndipo anazipereka kugula munda wa woumba mbiya, monga anandilamulira ine Ambuye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 ndipo anazipereka kugula munda wa woumba mbiya, monga anandilamulira ine Ambuye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 nagulira munda wa mmisiri wa mbiya, monga momwe Ambuye adaandilamulira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo anazigwiritsa ntchito kugula munda wa wowumba mbiya monga mmene Ambuye anandilamulira ine.” Onani mutuwo |