Mateyu 27:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo pakudza mamawa, ansembe aakulu ndi akulu a anthu onse anakhala upo wakumchitira Yesu, kuti amuphe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo pakudza mamawa, ansembe aakulu ndi akulu a anthu onse anakhala upo wakumchitira Yesu, kuti amuphe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 M'maŵa kutacha, akulu onse a ansembe ndi akulu a Ayuda adapanga upo kuti aphe Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mmamawa, akulu a ansembe onse ndi akuluakulu anavomerezana kuti aphe Yesu. Onani mutuwo |