Mateyu 26:66 - Buku Lopatulika66 muganiza bwanji? Iwo anayankha nati, Ali woyenera kumupha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201466 muganiza bwanji? Iwo anayankha nati, Ali woyenera kumupha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa66 Ndiye inu mukuganiza bwanji?” Iwo aja adayankha kuti, “Ayenera kuphedwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero66 Mukuganiza bwanji?” Iwo anayankha kuti, “Ayenera kuphedwa!” Onani mutuwo |