Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 26:62 - Buku Lopatulika

62 Ndipo mkulu wa ansembe anaimirira, nati kwa Iye, Suvomera kanthu kodi? Nchiyani ichi chimene awa akunenera Iwe?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

62 Ndipo mkulu wa ansembe anaimirira, nati kwa Iye, Suvomera kanthu kodi? Nchiyani ichi chimene awa akunenera Iwe?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

62 Tsono mkulu wa ansembe onse adaimirira nafunsa Yesu kuti, “Kodi ulibe poyankha? Nzotani zimene anthuŵa akukunenezazi?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

62 Pamenepo mkulu wa ansembe anayimirira nati kwa Yesu, “Kodi suyankha? Kodi umboni umenewu ndi otani umene anthu awa akupereka kukutsutsa Iwe?”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 26:62
7 Mawu Ofanana  

nati, Uyu ananena kuti, Ndikhoza kupasula Kachisi wa Mulunguyu, ndi kummanganso masiku atatu.


Koma Yesu anangokhala chete. Ndipo mkulu wa ansembe ananena kwa Iye, Ndikulumbiritsa Iwe pa Mulungu wamoyo, kuti utiuze ife ngati Iwe ndiwe Khristu, Mwana wa Mulungu.


Ndipo mkulu wa ansembe ananyamuka pakati, namfunsa Yesu, nanena, Suyankha kanthu kodi? Nchiyani ichi chimene awa alikuchitira mboni?


Ndipo anamfunsa Iye mau ambiri; koma Iye sanamyankhe kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa