Mateyu 26:59 - Buku Lopatulika59 Ndipo ansembe aakulu ndi akulu a milandu onse anafunafuna umboni wonama wakutsutsa Yesu, kuti amuphe Iye; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201459 Ndipo ansembe aakulu ndi akulu a milandu onse anafunafuna umboni wonama wakutsutsa Yesu, kuti amuphe Iye; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa59 Akulu a ansembe aja ndi onse a m'Bwalo Lalikulu la Ayuda ankafunafuna umboni wonama woneneza Yesu kuti amuphe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero59 Akulu a ansembe ndi akulu olamulira Ayuda amafunafuna umboni wonama wofuna kuphera Yesu. Onani mutuwo |