Mateyu 26:10 - Buku Lopatulika10 Koma Yesu podziwa, anati kwa iwo, Mumvutiranji mkaziyu? Popeza andichitira Ine ntchito yabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma Yesu podziwa, anati kwa iwo, Mumvutiranji mkaziyu? Popeza andichitira Ine ntchito yabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Yesu podziŵa zimene iwo aja ankalankhula, adaŵafunsa kuti, “Mukumuvutiranji maiyu? Zimenetu wandichitira iyeyuzi nzabwino kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yesu podziwa izi anawawuza kuti, “Chifukwa chiyani mukumuvutitsa mayiyu? Wandichitira Ine chinthu chabwino. Onani mutuwo |