Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 26:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau onse amenewa, anati kwa ophunzira ake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo panali pamene Yesu anatha mau onse amenewa, anati kwa ophunzira ake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Yesu atatsiriza kulankhula nkhani zonsezi, adauza ophunzira ake kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Yesu atamaliza kuyankhula zonsezi, anati kwa ophunzira ake,

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 26:1
3 Mawu Ofanana  

Ndipo panali pamene Yesu anatha mau amenewa, anachokera ku Galileya, nadza ku malire a Yudeya, a ku tsidya lija la Yordani.


Ndipo panakhala pamene Yesu anatha mau amenewa, makamu a anthu anazizwa ndi chiphunzitso chake:


Koma Paska wa Ayuda anali pafupi; ndipo ambiri anakwera kunka ku Yerusalemu kuchoka kuminda, asanafike Paska, kukadziyeretsa iwo okha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa