Mateyu 25:9 - Buku Lopatulika9 Koma ochenjera anayankha nati, Kapena sangakwanire ife ndi inu; koma makamaka mukani kwa ogulitsa malonda, mukadzigulire inu nokha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma ochenjera anayankha nati, Kapena sangakwanire ife ndi inu; koma makamaka mukani kwa ogulitsa malonda, mukadzigulire inu nokha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma ochenjera aja adati, ‘Hi, ai, tikatero satikwanira tonsefe. Bwanji osati mungopita ku sitoro mukagule anu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Ochenjerawo anayankha, nati, ‘Ayi sangakwanire inu ndi ife. Pitani kwa ogulitsa mafuta ndi kukadzigulira nokha.’ Onani mutuwo |