Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 24:32 - Buku Lopatulika

32 Koma phunzirani ndi mkuyu fanizo lake; pamene tsopano nthambi yake ili yanthete, niphuka masamba ake, muzindikira kuti dzinja liyandikira;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Koma phunzirani ndi mkuyu fanizo lake; pamene tsopano nthambi yake ili yanthete, niphuka masamba ake, muzindikira kuti dzinja liyandikira;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 “Yang'anani mkuyu kuti mutengerepo phunziro. Mukamaona kuti nthambi zake zayamba kukhala zanthete, ndipo masamba akuphuka, mumadziŵa kuti chilimwe chayandikira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 “Tsopano kuchokera ku mtengo wamkuyu phunzirani ichi: Pamene uyamba kuphukira, masamba ake akatuluka, mumadziwa kuti dzinja layandikira.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 24:32
5 Mawu Ofanana  

Mkuyu utchetsa nkhuyu zake zosakhwima, mipesa niphuka, inunkhira bwino. Tauka, bwenzi langa, wokongola wangawe, tiyetu.


Ndipo Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwakukulu kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa osankhidwa ake kumphepo zinai, kuyambira malekezero a thambo kufikira malekezero ake ena.


chomwechonso inu, pamene mudzaona zimenezo, zindikirani kuti Iye ali pafupi, inde pakhomo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa