Mateyu 24:26 - Buku Lopatulika26 Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko. Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 “Nchifukwa chake, anthu akadzakuuzani kuti, ‘Inu, Khristu ali ku chipululu,’ musadzapiteko. Kapena akadzati, ‘Ali m'kati mwa nyumba,’ musadzakhulupirire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “Ndiye ngati wina akuwuzani inu kuti, ‘Uyo ali ku chipululu,’ inu musapiteko; kapena akati, ‘Uyu ali kuno mʼchipinda chamʼkati,’ musakhulupirire. Onani mutuwo |