Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 24:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo pempherani kuti kuthawa kwanu kusakhale pa nyengo yachisanu, kapena pa Sabata;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo pempherani kuti kuthawa kwanu kusakhale pa nyengo yachisanu, kapena pa Sabata;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Pempherani kuti nthaŵi pamene muzidzathaŵa, isadzakhale nyengo yachisanu, kapena pa tsiku la Sabata.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Pempherani kuti kuthawa kwanu kusadzachitike nthawi yozizira kapena pa Sabata.

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 24:20
4 Mawu Ofanana  

Taonani, popeza Yehova anakupatsani Sabata, chifukwa chake tsiku lachisanu ndi chimodzi alikupatsa inu mkate wofikira masiku awiri; khalani yense m'malo mwake munthu asatuluke m'malo mwake tsiku lachisanu ndi chiwiri.


Koma tsoka ali nalo iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana m'masiku awo!


pakuti pomwepo padzakhala masauko aakulu, monga sipadakhale otero kuyambira chiyambi cha dziko, kufikira tsopano, inde ndipo sipadzakhalanso.


Pamenepo anabwera ku Yerusalemu kuchokera kuphiri lonenedwa la Azitona, limene liyandikana ndi Yerusalemu, loyendako tsiku la Sabata.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa