Mateyu 24:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yesu anatuluka ku Kachisi; ndipo ophunzira ake anadza kudzamuonetsa chimangidwe cha Kachisiyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yesu anatuluka ku Kachisi; ndipo ophunzira ake anadza kudzamuonetsa chimangidwe cha Kachisiyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu adatuluka m'Nyumba ya Mulungu, ndipo pamene ankachoka, ophunzira ake adabwera nkumamuwonetsa kamangidwe ka Nyumbayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yesu anatuluka mʼNyumba ya Mulungu ndipo akuchoka ophunzira ake anadza kwa Iye ndi kumuonetsa mamangidwe a Nyumbayo. Onani mutuwo |