Mateyu 23:6 - Buku Lopatulika6 nakonda malo a ulemu pamaphwando, ndi mipando ya ulemu m'masunagoge, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 nakonda malo a ulemu pamaphwando, ndi mipando ya ulemu m'masunagoge, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Amakonda malo olemekezeka pa maphwando ndiponso mipando yaulemu kwambiri ku nyumba zamapemphero. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Amakonda malo aulemu pa maphwando ndi malo ofunika kwambiri mʼmasunagoge. Onani mutuwo |