Mateyu 22:9 - Buku Lopatulika9 Chifukwa chake pitani inu kumphambano za njira, ndipo aliyense amene mukampeze, itanani kuukwatiku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chifukwa chake pitani inu kumphambano za njira, ndipo amene aliyense mukampeze, itanani kuukwatiku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pitani tsono ku mphambano za miseu, mukaitane aliyense amene mukampeze, kuti abwere kuno ku phwando laukwati.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pitani ku mphambano za misewu ndipo kayitaneni aliyense amene mukamupeze kuti abwere ku phwando.’ Onani mutuwo |