Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 22:36 - Buku Lopatulika

36 Mphunzitsi, lamulo lalikulu ndi liti la m'chilamulo?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Mphunzitsi, lamulo lalikulu ndi liti la m'chilamulo?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Adati, “Aphunzitsi, kodi mwa malamulo onse a Mulungu, lalikulu ndi liti?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 “Aphunzitsi, kodi lamulo lalikulu koposa mu malamulo ndi liti?”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 22:36
8 Mawu Ofanana  

Ndinamlembera zinthu zambirimbirizo za chilamulo changa, koma zinayesedwa ngati chinthu chachilendo.


iyeyo sadzalemekeza atate wake. Ndipo inu mupeputsa mau a Mulungu chifukwa cha miyambo yanu.


Ndipo mmodzi wa iwo, mphunzitsi wa malamulo, anamfunsa ndi kumuyesa Iye, nati,


Ndipo Yesu anati kwa iye, Uzikonda Ambuye Mulungu wako ndi mtima wako wonse, ndi moyo wako wonse, ndi nzeru zako zonse.


Koma tsoka inu, Afarisi! Chifukwa mupereka limodzi la magawo khumi la timbeu tonunkhira, ndi timbeu tokometsa chakudya ndi ndiwo zonse, ndipo mumaleka chiweruzo ndi chikondi cha Mulungu; mwenzi mutachita izi, ndi kusasiya zinazo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa