Mateyu 22:23 - Buku Lopatulika23 Tsiku lomwelo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; namfunsa Iye, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Tsiku lomwelo anadza kwa Iye Asaduki, amene amanena kuti palibe kuuka kwa akufa; namfunsa Iye, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Tsiku lomwelo Asaduki ena adadza kwa Yesu. (Paja iwo amati akufa sadzauka.) Adamufunsa kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Tsiku lomwelo Asaduki amene amati kulibe za kuukanso, anabwera kwa Iye ndi funso. Onani mutuwo |