Mateyu 22:12 - Buku Lopatulika12 nanena kwa iye, Mnzangawe, unalowa muno bwanji wosakhala nacho chovala cha ukwati? Ndipo iye analibe mau. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 nanena kwa iye, Mnzangawe, unalowa muno bwanji wosakhala nacho chovala cha ukwati? Ndipo iye analibe mau. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono idamufunsa kuti ‘Kodi iwe, waloŵa bwanji muno opanda chovala chaukwati?’ Iye uja adangoti chete. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Inamufunsa kuti, ‘Bwenzi walowa bwanji muno wopanda zovala zaukwati?’ Munthuyo anakhala chete. Onani mutuwo |