Mateyu 21:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo ichi chinatero, kuti chikachitidwe chonenedwa ndi mneneri kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo ichi chinatero, kuti chikachitidwe chonenedwa ndi mneneri kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Zimenezi zidaatero kuti zipherezere zimene mneneri adaanena kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Izi zinachitika kukwaniritsa zimene zinayankhulidwa ndi mneneri: Onani mutuwo |