Mateyu 21:26 - Buku Lopatulika26 Koma tikati, Kwa anthu, tiopa khamulo la anthu; pakuti onse amuyesa Yohane mneneri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Koma tikati, Kwa anthu, tiopa khamulo la anthu; pakuti onse amuyesa Yohane mneneri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Komanso tikati adaazitenga kwa anthu, anthuŵa satileka, chifukwatu onse amati Yohane anali mneneri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Koma tikati, ‘Kuchokera kwa anthu,’ ife tikuopa anthuwa, pakuti onse amakhulupirira kuti Yohane anali mneneri.” Onani mutuwo |