Mateyu 21:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anadza kwa Iye ku Kachisiko akhungu ndi opunduka miyendo, nachiritsidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anadza kwa Iye ku Kachisiko akhungu ndi opunduka miyendo, nachiritsidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Anthu akhungu ndi opunduka adadza kwa Yesu m'Nyumba ya Mulungumo, ndipo Iye adaŵachiritsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Anthu osaona ndi olumala anabwera kwa Iye mʼNyumba ya Mulungu ndipo anawachiritsa. Onani mutuwo |