Mateyu 20:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo pamene iwo olembedwa poyandikira madzulo anadza, analandira munthu aliyense rupiya latheka limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo pamene iwo olembedwa poyandikira madzulo anadza, analandira munthu aliyense rupiya latheka limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pamene adabwera olembedwa pa 5 koloko yamadzulo aja, aliyense adalandira ndalama imodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Antchito amene anawalemba ganyu pa 5 koloko masana anafika ndipo aliyense analandira dinari. Onani mutuwo |