Mateyu 20:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo m'mene oyamba anadza, analingalira kuti adzalandira kopambana, ndipo iwonso analandira onse rupiya latheka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo m'mene oyamba anadza, analingalira kuti adzalandira kopambana, ndipo iwonso analandira onse rupiya latheka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono pamene olembedwa poyamba aja adabwera, ankaganiza kuti alandira pakulu. Koma nawonso adangolandira aliyense ndalama imodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo atabwera kwa amene analembedwa poyamba anayembekezera kuti alandira zambiri. Koma aliyense wa iwo analandira dinari. Onani mutuwo |