Mateyu 20:20 - Buku Lopatulika20 Pomwepo anadza kwa Iye amake a ana a Zebedeo ndi ana ake omwe, namgwadira, ndi kumpempha kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pomwepo anadza kwa Iye amake a ana a Zebedeo ndi ana ake omwe, namgwadira, ndi kumpempha kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pambuyo pake mkazi wa Zebedeo adadza ndi ana ake kwa Yesu, namgwadira kuti ampemphe kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Amayi a ana a Zebedayo anabwera ndi ana ake kwa Yesu, nagwada pansi namupempha Iye. Onani mutuwo |