Mateyu 20:1 - Buku Lopatulika1 Pakuti Ufumu wa Kumwamba ufanana ndi munthu mwini banja, amene anatuluka mamawa kukalembera antchito a m'munda wake wampesa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pakuti Ufumu wa Kumwamba ufanana ndi munthu mwini banja, amene anatuluka mamawa kukalembera antchito a m'munda wake wampesa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 “Za Ufumu wakumwamba tingazifanizire motere: Munthu wina adaalaŵirira m'mamaŵa kukalemba anthu okagwira ntchito m'munda wake wamphesa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 “Ufumu wakumwamba uli ngati mwini munda amene anapita mmawa kukalemba anthu aganyu kuti akagwire ntchito mʼmunda wake wa mpesa. Onani mutuwo |