Mateyu 2:7 - Buku Lopatulika7 Pomwepo Herode anawaitana Anzeruwo m'tseri, nafunsitsa iwo nthawi yake idaoneka nyenyeziyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pomwepo Herode anawaitana Anzeruwo m'tseri, nafunsitsa iwo nthawi yake idaoneka nyenyeziyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Pamenepo Herode adaŵaitanira paseri akatswiri a nyenyezi aja, naŵafunsitsa za nthaŵi yeniyeni imene adaaiwonera nyenyeziyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Pomwepo Herode anawayitanira mseri Anzeruwo nawafunsitsa nthawi yeniyeni yomwe nyenyeziyo inaoneka. Onani mutuwo |