Mateyu 2:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo iwo poona nyenyeziyo, anakondwera ndi kukondwera kwakukulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo iwo poona nyenyeziyo, anakondwera ndi kukondwera kwakukulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ataiwona nyenyeziyo, adasangalala kwabasi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pamene iwo anaona nyenyeziyo, anasangalala kwambiri. Onani mutuwo |