Mateyu 19:18 - Buku Lopatulika18 Iye ananena kwa Iye, Otani? Ndipo Yesu anati, Usaphe, Usachite chigololo, Usabe, Usachite umboni wonama, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Iye ananena kwa Iye, Otani? Ndipo Yesu anati, Usaphe, Usachite chigololo, Usabe, Usachite umboni wonama, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Iye adati, “Malamulo ake oti?” Yesu adayankha kuti, “Usaphe, usachite chigololo, usabe, usachite umboni wonama, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mnyamatayo anamufunsa kuti, “Ndi ati?” Yesu anayankha kuti, “Usaphe, usachite chigololo, usabe, usapereke umboni onama, Onani mutuwo |