Mateyu 18:4 - Buku Lopatulika4 Chifukwa chake yense amene adzichepetsa yekha monga kamwana aka, yemweyo ali wopambana mu Ufumu wa Kumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Chifukwa chake yense amene adzichepetsa yekha monga kamwana aka, yemweyo ali wopambana mu Ufumu wa Kumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Nchifukwa chake munthu wodzichepetsa ngati mwana uyu, ameneyo ndiye wamkulu mu Ufumu wakumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Chifukwa chake, aliyense amene adzichepetsa yekha ngati kamwana aka, ameneyo ndiye wamkulu koposa onse mu ufumu wakumwamba. Onani mutuwo |