Mateyu 18:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo mbuye wake anakwiya, nampereka kwa azunzi, kufikira akambwezere iye mangawa onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo mbuye wake anakwiya, nampereka kwa azunzi, kufikira akambwezere iye mangawa onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Motero mbuye wakeyo adapsa mtima kwambiri, nampereka kuti akamzunze mpaka atabweza ngongole yonse ija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ndi mkwiyo, bwana wakeyo anamupereka kwa oyangʼanira ndende kuti amuzuze mpaka atabweza zonse zimene anakongola. Onani mutuwo |