Mateyu 18:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo iye sanafune; koma anamuka, namponya iye m'nyumba yandende, kufikira abwezere ngongole. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo iye sanafune; koma anamuka, namponya iye m'nyumba yandende, kufikira abwezere ngongole. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Koma iye adakana, nakamponyetsa m'ndende kuti mpaka abweze ndithu ngongoleyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 “Koma iye anakana. Mʼmalo mwake, anachoka nakamumangitsa kufikira atabweza ngongoleyo. Onani mutuwo |