Mateyu 18:26 - Buku Lopatulika26 Chifukwa chake kapoloyo anagwada pansi, nampembedzera, nati, Mbuye, bakandiyembekezani ine, ndipo zonse ndidzazibwezera kwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Chifukwa chake kapoloyo anagwada pansi, nampembedzera, nati, Mbuye, bakandiyembekezani ine, ndipo zonse ndidzazibwezera kwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Apo wantchito uja adamgwadira nati, ‘Pepani, ndakupembani, lezereni mtima, ndidzakubwezerani ndithu zonse.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “Wantchitoyo anagwada pamaso pake namupempha iye kuti, ‘Lezereni mtima ndipo ndidzabweza zonse.’ Onani mutuwo |