Mateyu 18:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo mbuye wa kapoloyo anagwidwa ndi chisoni mumtima, nammasula iye, namkhululukira ngongole. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo mbuye wa kapoloyo anagwidwa ndi chisoni mumtima, nammasula iye, namkhululukira ngongole. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Mbuye wake uja adamumveradi chifundo, ndipo adamkhululukira ngongole ija, namlola kuti apite. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Bwana wakeyo anamuchitira chifundo, namukhululukira ngongoleyo ndipo anamulola apite. Onani mutuwo |