Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mateyu 18:21 - Buku Lopatulika

21 Pamenepo Petro anadza, nati kwa Iye, Ambuye, mbale wanga adzandilakwira kangati, ndipo ine ndidzamkhululukira iye? Kufikira kasanu ndi kawiri kodi?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Pamenepo Petro anadza, nati kwa Iye, Ambuye, mbale wanga adzandilakwira kangati, ndipo ine ndidzamkhululukira iye? Kufikira kasanu ndi kawiri kodi?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Pamenepo Petro adadzafunsa Yesu kuti, “Ambuye, kodi mbale wanga atamandichimwira, ndidzamkhululukire kangati? Kodi ndidzachite kufikitsa kasanunkaŵiri?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Kenaka Petro anabwera kwa Yesu ndi kumufunsa kuti, “Ambuye, kodi mʼbale wanga akandichimwira ndimukhululukire kokwanira kangati? Mpaka kasanu nʼkawiri?”

Onani mutuwo Koperani




Mateyu 18:21
2 Mawu Ofanana  

Ndipo ngati mbale wako akuchimwira iwe, pita, numlangize pa nokha iwe ndi iye; ngati akumvera iwe, wambweza mbale wako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa