Mateyu 17:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo pamene ophunzira anamva, anagwa nkhope zao pansi, naopa kwakukulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo pamene ophunzira anamva, anagwa nkhope zao pansi, naopa kwakukulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ophunzira aja atamva zimenezi, adachita mantha kwambiri nadzigwetsa chafufumimba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ophunzira atamva zimenezi, anachita mantha nagwa pansi chafufumimba. Onani mutuwo |