Mateyu 17:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo ophunzira ake anamfunsa, nanena, Ndipo bwanji alembi amanena kuti Eliya ndiye atsogole kudza? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo ophunzira ake anamfunsa, nanena, Ndipo bwanji alembi amanena kuti Eliya ndiye atsogole kudza? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ophunzira aja adamufunsa kuti, “Nanga bwanji aphunzitsi a Malamulo amati Eliya adzayenera kuyamba wabwera?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ophunzira anamufunsa Iye kuti, “Nanga nʼchifukwa chiyani aphunzitsi amalamulo amati Eliya ayenera kukhala woyamba kubwera?” Onani mutuwo |