Mateyu 16:25 - Buku Lopatulika25 Pakuti iye amene afuna kupulumutsa moyo wake adzautaya: koma iye amene ataya moyo wake chifukwa cha Ine, adzaupeza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pakuti iye amene afuna kupulumutsa moyo wake adzautaya: koma iye amene ataya moyo wake chifukwa cha Ine, adzaupeza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Chifukwa wofuna kupulumutsa moyo wake, adzautaya, koma wotaya moyo wake chifukwa cha Ine, adzaupeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pakuti aliyense amene afuna kupulumutsa moyo wake adzawutaya koma aliyense amene ataya moyo wake chifukwa cha Ine adzawupeza. Onani mutuwo |