Mateyu 16:2 - Buku Lopatulika2 Koma Iye anayankha, nati kwa iwo, Madzulo munena, Kudzakhala ngwee; popeza thambo lili lacheza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma Iye anayankha, nati kwa iwo, Madzulo munena, Kudzakhala ngwee; popeza thambo lili lacheza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma Yesu adaŵauza kuti, “Pamene dzuŵa likuloŵa, mumati, ‘Maŵa kucha bwino, popeza kuti kumwamba kuli psuu.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anayankha kuti, “Kunja kukamada, inu mumati, kudzakhala nyengo yabwino popeza thambo ndi lofiira. Onani mutuwo |