Mateyu 16:15 - Buku Lopatulika15 Iye ananena kwa iwo, Koma inu mutani kuti Ine ndine yani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Iye ananena kwa iwo, Koma inu mutani kuti Ine ndine yani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Apo Yesu adaŵafunsa kuti, “Nanga inuyo, mumati ndine yani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Iye anafunsa kuti, “Nanga inuyo mumati ndine yani?” Onani mutuwo |