Mateyu 15:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Muli nayo mikate ingati? Ndipo iwo anati, Isanu ndi iwiri, ndi tinsomba pang'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Muli nayo mikate ingati? Ndipo iwo anati, Isanu ndi iwiri, ndi tinsomba pang'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Yesu adaŵafunsa kuti, “Kaya buledi muli naye mngati?” Iwo aja adati, “Msanu ndi muŵiri, ndiponso tinsomba toŵerengeka.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Yesu anawafunsa kuti, “Muli ndi malofu a buledi angati?” Iwo anayankha kuti, “Asanu ndi awiri ndi tinsomba pangʼono.” Onani mutuwo |