Mateyu 15:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo Iye analamulira anthuwo akhale pansi onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo Iye analamulira anthuwo akhale pansi onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Apo Yesu adalamula anthu aja kuti akhale pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Iye anawuza gululo kuti likhale pansi. Onani mutuwo |