Mateyu 15:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo ophunzira ananena kwa Iye, Tiione kuti mikate yotere m'chipululu yakukhutitsa unyinji wotere wa anthu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo ophunzira ananena kwa Iye, Tiione kuti mikate yotere m'chipululu yakukhutitsa unyinji wotere wa anthu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Ophunzirawo adamufunsa kuti, “Anthu ochuluka chotereŵa tingaŵapezere kuti chakudya chokwanira, kuthengo ngati kuno?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Ophunzira anayankha kuti, “Ndikuti kumene tingakapeze buledi mʼtchire muno okwanira kudyetsa gulu lotere?” Onani mutuwo |