Mateyu 14:1 - Buku Lopatulika1 Nthawi imeneyo Herode mfumu anamva mbiri ya Yesu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Nthawi imeneyo Herode mfumu anamva mbiri ya Yesu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pa nthaŵi imeneyo Herode, mfumu ya ku Galileya, adaamva zimene anthu ankanena za Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pa nthawi imeneyo Mfumu Herode anamva za mbiri ya Yesu. Onani mutuwo |