Mateyu 13:58 - Buku Lopatulika58 Ndipo Iye, chifukwa cha kusakhulupirira kwao, sanachite kumeneko zamphamvu zambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201458 Ndipo Iye, chifukwa cha kusakhulupirira kwao, sanachite kumeneko zamphamvu zambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa58 Motero sadachite zamphamvu zambiri kumeneko, chifukwa cha kusakhulupirira kwa anthuwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero58 Ndipo Iye sanachite zodabwitsa zambiri kumeneko chifukwa cha kusowa kwa chikhulupiriro kwawo. Onani mutuwo |