Mateyu 13:53 - Buku Lopatulika53 Ndipo panali, pamene Yesu anatha mafanizo awa, anachokera kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Ndipo panali, pamene Yesu anatha mafanizo awa, anachokera kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Yesu atatsiriza kunena mafanizoŵa, adachoka kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Yesu atatsiriza mafanizowa anachoka kumeneko. Onani mutuwo |