Mateyu 13:50 - Buku Lopatulika50 nadzawataya m'ng'anjo yamoto; komweko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 nadzawataya m'ng'anjo yamoto; komweko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 nkumaŵaponya m'ng'anjo ya moto. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Ndipo oyipa adzawaponya mʼngʼanjo ya moto kumene kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.” Onani mutuwo |