Mateyu 13:34 - Buku Lopatulika34 Zonsezi Yesu anaziphiphiritsira m'mafanizo kwa makamu a anthu; ndipo kopanda fanizo sanalankhule kanthu kwa iwo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Zonsezi Yesu anaziphiphiritsira m'mafanizo kwa makamu a anthu; ndipo kopanda fanizo sanalankhule kanthu kwa iwo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Zonsezi Yesu adalankhula ndi anthu aja m'mafanizo. Sadalankhule nawo kanthu popanda fanizo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Yesu anayankhula zinthu zonsezi kwa gulu la anthu mʼmafanizo ndipo Iye sananene kalikonse kwa iwo osagwiritsa ntchito fanizo. Onani mutuwo |